Mwitiya, Machinga
Mwitiya ni malo agho ghakusangika mu boma la Machinga,chigaŵa cha kummwela,mu charu cha Malaŵi. mwitiya simfumu yayikulu ikafika pamanso pa mfumu Sale. Koma ndi Dzina lokhalo lomwe limagwiritsidwa ntchito Ndi anthu ochokera m'delali, komanso lim'kagwiritsidwa kuyambira kale. ndipo dzinali lidali lom'veka kwambiri kuyambira makezana kufikira pomwe mfumu yayikulu Nyambi inagawira m'bale wake [Sale] delali Kuti azilamulila. Mafumu amene azungulila afumuwa azungulilidwa ndimafumu azawo Monga amatwaya,amororah,abwana, abisa,akowa,akwepu,amasale,akalimele ,andindi,atonda,athiniwa , adailess,amakina,atapula,kutapasya,adoka ,amonjeza,kugalama,akatuma,apuluma,alimamu,atambala akazembe , ndi ena ambiri m'delali. ndipo amene ali pakati pa Mwitiya ndi Malundani ndimonga alikaka, amongola, ku'mlanda, kum'lanje, akonde, abakali, komanso atali. [[ mwitiya siili patali kwenikweni kuchoka Kumalundani kwawo Kwa , [[Max P Spark, artist Koma ndi mtunda wa 9.5 km amangovuta ndimayendedwe basi chifukwa chamaphiri. Quick fact about their culture
Machinga
Bakhili • Balaka • Chabwera • Chakhame • Chibwana • Chidothe • Chikojo • Chikuluma • Chikumba • Chikuwita • Chikweo • Chilala • Chilemba • Chilolo • Chimala • Chimanda • Chimbila • Chimbwanya • Chimombo, Machinga • Chindamba • Chinguwo, Machinga • Chinguza • Ching’oma, Machinga • Chipanda, Machinga • Chipolonga, Machinga • Chisawa • Chisiza • Chisuse, Machinga • Chisuwi • Chitenjere,Machinga • Chitundu • Chiuja • Chiwalo • Chiwambo • Cilala • Dinje • Ekhama • Halala, Machinga • Idi • Issa, Machinga • Jambo, Machinga • Juma • Kakutu, Machinga • Kalambo, Machinga • Kalenga, Machinga • Kamala, Machinga • Kapoloma, Machinga • Kasupe, Machinga • Katolokoso, Machinga • Kaugule • Kawa, Machinga • Kawelama • Kawinga, Machinga • Khuzumba, Machinga • Kokoti • Kolopa • Kungwa • Lambulila • Likhonyowa • Liwonde • Lulanga • Lulanga • Macece • Maceka • Macepa • Machina • Macilinga • Magwila • Mahata • Majaja • Makata • Makoka • Makome • Makwakwa • Makwemba • Malango • Maleta • Maluma • Malupi • Maniwa • Maniya • Mapata • Mapila • Masaka, Machinga • Masese, Machinga • Mataka, Machinga • Maunda, Machinga • Maweha, Machinga • Mayese,Machinga • Mbalame, Machinga • Mbalwe, Machinga • Mbawa, Machinga • Mbwezo,Machinga • Mijombo • Milaza, Machinga • Milimbo, Machinga • Misi,Machinga • Mkula, Machinga • Mkweya,Machinga • Mlomba, Machinga • Mmeta, Machinga • Mongora, Machinga • Moro, Machinga • Mowere,Machinga • Mpakaka • Mpalume • Mpheta, Machinga • Mphonde,Machinga • Mponda, Machinga • Mposa, Machinga • Mpotola, Machinga • Mpumbe, Machinga • Mpunga • Msope,Machinga • Mteuka • Mthiniwa,Machinga • Mtonda, Machinga • Mtundu, Machinga • Muepetha, Machinga • Muhara, Machinga • Muhatele, Machinga • Mula, Machinga • Mundi • Muwawa, Machinga • Mwala • Mwalija, Machinga • Mwambala, Machinga • Mwanje, Machinga • Mwegama, Machinga • Mweny, Machinga • Mwenye, Machinga • Mwila, Machinga • Mwili, Machinga • Mwitiya, Machinga • Namanja, Machinga • Namikango • Nampeya • Namuku • Namwini, Machinga • Nanganga, Machinga • Nantwe, Machinga • Naphome, Machinga • Naphuthu, Machinga • Nawanga, Machinga • Nayuci, Machinga • Nchelela • Ncimbo • Ncokola, Machinga • Ndamba • Ndambala, Machinga • Ndenda, Machinga • Nepiyala, Machinga • Ngokwe,Machinga • Ngomano, Machinga • Ngongondo • Nkaku • Nkalama • Nkapa, Machinga • Nkhokwe • Nkisa • Nkoko, Machinga • Nkotama,Machinga • Nkwanda,Machinga • Nkwila • Nlaluwele • Nlamba • Nlambalala • Nlawa • Nlungu, Machinga • Nluwila, Machinga • Nsanama,Machinga • Nsanyila • Nsonde, Machinga • Nsume • Ntaja, Machinga • Ntali • Ntila • Ntolowa • Ntungwi, Machinga • Nyambi, Machinga • Nyandule • Nyangatayani, Machinga • Nyanje, Machinga • Nyanya • Nyanyika, Machinga • Nyenga • Nyenje • Phwiti • Pingo • Pitiya • Pondelani, Machinga • Puruma • Saidi • Saleya • Samu, Machinga • Sangula • Sani • Sawanje • Siwala • Sombo • Sulumba • Tanthauko • Thawale • Thomo • Umpuanela • Wethiwa • Zilale
ndi dela limene limapezeka anthu awulemu ndi ozichepetsa pamakhalidwe awo, ambiri mwa Iwo ndiamtundu wachi hlomwe, Koma amapanga zachikhalidwe cha chiyao ndipo mwadzina kuli Namtongwe, Jando, lupanda, mtsondo ndi Zina amene sadutsa kumalilo amamugwira ndikumumanga kumanda.ndipo okwela njinga pa malilo amakwizingidwa kufikila anthu abalalike. izi zimachitika polimbikitsa chikhalidwe ndikumanga umodzi kutukuka [[delali limapezekela kumwela Kwa dziko la Malawi boma la Machinga ndi dela lokhalo lotsangalatsa Maka Ku nkhani yachilengedwe komanso maphiri atali atali. ndidelanso lomwe limadalila ulimi kwambiri,ndichifukwa anthu ake adatukuka kuyambila Zaka zam'mbuyomu]]. mwitiya ili kuseli Kwa phiri la Lisale tikamachoka Ku Malundani, Kwa mfumu yayikulu Nyambi kungopitilila kuchoka Kwa amwitiya kumapita Kwa a Molorah mkukapitilila kwam'tonda kenako m'sinje wa Chipumulisi kudutsa Kandulu farm, umakatulukila Kum'kwakwata komwe nditsika omaliza Malo omaliza a Malawi Mbali imeneyi. kenako umadzalowa dziko lina la Mozambique Koma Ngati ungakhote kumanja umadzapitilila mpaka Kwa T/A m'Ngokwe.