Malundani, Machinga
Kaonekelo
Malundani ni malo agho ghakusangika mu boma la Machinga,chigaŵa cha kummwela,mu charu cha Malaŵi. Malo abwino kukhala kuposa Malo onse amene akupezeka m'boma la Machinga. Malundani ndi dela lomwe Likupezeka Kwa Mfumu yayikulu Nyambi. komanso mafumu ang'ono ang'ono, Monga Nasolola,Chitanganya,M'topole,Mlenje,Maisi,Dulamu, komanso Mchika. Kumalundani kuli zonse zoyeneleza umoyo wa anthu. kuli madambo abwino,maphiri ataliatali abwinonso Monga ulongwe,Lisale,chigweje, ndimaphiri ena ozungulira. kuli zotsangalatsa zambiri komanso anyamata alunso Monga Max P Spark, Justine Chiwambo, Criemo ndi ena ambiri. Malundani.